A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z #

NATHAN CHIKOYA lyrics : "LIMBIKIRA"

CGAmFG
This song is for every one who's going through a struggle Limbikira..
Verse 1

Pamene Atate anga anatisiya ndinaona monga dziko landitera.
Koma Amai !@#^imbika kutisunga sanasiye kundilimbitsa,
Mwana wanga ukonde sikulu usewenze ndimanja ako!!

Chorus
Mwana wanga Limbikira mwana wanga umoyo n@#$%ondo,
Ukacita ulesi uzadya maudzu mwana wanga limbikira.

Mwana wanga Limbikira mwana wanga umoyo n@#$%ondo,
Ukacita ulesi uzadya maudzu mwana wanga limbikira.
Verse 2

Ndika!@$&bukira mau ya Amai ndimagwada ndiyamika Mulungu,
Pamau anu olimbitsa mau anu opatsa nzelu.
Ndipamene ndipedza zolimba zamudziko ndi!@$&bukira mau anu akuti!!!

Rap
Yeah!! It doesn't feel so bad I was just like you
I used to wake up with no food just like you

I lost my daddy just like you
But that has got none to do with you men
All you have to do is hold on and be strong pray to God

He watches over you 'cause he will never leave your side, never leave your side!!!

Submit Corrections