A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z #

NATHAN CHIKOYA lyrics : "Tiyenera Kukukondani"

[Verse 1]
[C Am F G]
Mwandivutikira pamtandapo kulibe wina monga inu.

Ndinyenera kukukwezani kulibe wina monga inu,
Ine ndi abale anga mwatikonzera njira, njira yabwino.
Tiyenera kukukondani, tiyenera kukukondani.

Tiyenera kukukondani, tiyenera kukukondani.

[Chorus]

Kulibe wina monga inu Mulungu wathu, kulibe wina monga inu Ambuye Yesu.
Kulibe wina monga inu Mulungu wathu, kulibe wina monga inu Ambuye Yesu.
Tiyenera kukukondani, tiyenera kukukondani,

tiyenera kukukondani, tiyenera kukukondani.

[Verse 2]

Mawe mawe wavutika mwanawankosa chi!@*@wa change ine.
Ume!! ume !mawe! mawe! Yesu wavutikiranji
Eli !Eli! akesa mwadzi wake chi!@*@wa cha ine.

Wandiyeretsa wandipatsa moyo ndiyenera kukukondani,
Wandiyeretsa wandipatsa moyo ndiyenera kukukondani.


[Verse 3]
Kana ndiri naco chuma chadziko lapansi
Ndingacitaye chi!@*@wa chachikondi chake chandipatsa moyo.

Ndinyadira pamtandapo pomwe anandifera Yesu
Mwini wamoyo kutaya moyo wake chi!@*@wa chaine. (Anakesedwa mwadzi)


[Ending]
Chi!@*@wa chaine, chi!@*@wa chaine, chi!@*@wa chaine, chi!@*@wa chaine.
[Repeat twice]

Submit Corrections