A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z #

NATHAN CHIKOYA lyrics : "Tidzakaonana - The Tribute"

[Intro]
[GEmCD]
This is a tribute to my dad and my brother John

Rest in peace.

[Verse 1]

Amai anga mutsalire ndiimfa ya amuna anu
Amai anga mutsalire ndiimfa ya mwana wanu.
Okufa MwaYesu alinawo moyo wina

Mtima ungasweke kulira mngalire koma chimodzi ndidziwa.

[Chorus]

Tidzakaonana futi Yesu pakubwera, Tidzakaonana futi Yesu pakubwera.
Tidzakaonana futi Yesu pakubwera, Tidzakaonana futi Yesu pakubwera.


[Verse 2]
Imfa iwe imfa ulibe chifundo Imfa iwe imfa watenga abale anga.
Ukutodola anthu umedza suukuta

Koma manyadzi kwaiwe Yesu akugonjetsa,
Koma manyadzi kwaiwe Yesu akugonjetsa.


[Verse 3]
Kukondwa komweko imfa kulibe,
Ndinyimbo yasopano tidzaimba kosaleka.

Alleluya, Alleluya, imfa wagonja, Alleluya, Alleluya, imfa wagonja.
Alleluya, Alleluya, imfa wagonja, Alleluya, Alleluya, imfa wagonja.

Submit Corrections