A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z #

MASKAL lyrics : "Ndiwe Wanga"

Verse; 1
Pazachikondi chako dziwa ine ndi mboni
Sindinalakelake kupita ku Joni

Chikondi cha iwe ndi ine sicham'mafoni
Nchi!@*@wa sindinapite ku bank kukatenga loan
Chikondi chathu chobeba chanoninoni

Umandizula moyo ukapereka moni
Umandi!@$&butsa za kwathu !@$&angoni
Ndakondwa umadziwa kuti ine ndi m'goni


Chorus*2
Ndiwe wanga ndiwe kuwala kwanga

Ndiwe wanga ndiwe nyenyezi yanga
Ndiwe wanga ndiwe wanga ndiwe wapamtima wanga
Ndiwe wanga ndiwe wanga nyenyezi yanga

Ndiwe wanga ndiwe kuwala kwanga

Verse; 2

Ndikakha pansi ndimadziwa ndiri ndi mzanga
Kuyenda limodzi tifanana mawanga
Amandinena ati ndiri nyanga

Asatilongoze monga ichita nkhanga
Ndithudi ndilonjeza ndzakutengela kunyanja
Nthawi imeneyo tikukonzekera banja

Ona ambiri akutiombera m'manja
Mpakana wena kutimangira nsanja


(Back to chorus)

Verse; 3

Chikondi chathu chansangala sizachisoni
Ena amasangalala akatipatsa moni
Unasiya amabenzi onse ndimalinkoni

Amatithila madzi ndi!@$&aimba horn
Akamaditsa baby, Samamvetsa baby
Ngati andale baby, Ali pa njale baby

Zimawawawa baby, Kuiwala mawa baby
Ngati moyenda baby, Ife tikuyenda baby!, Hee!


(Back to chorus till the end)


Submit Corrections