A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z #

LANGWAN PIKSY lyrics : "Maloto"

VERSE 1
I saw mwana wanga
What a cute baby

Proud dad anzanga anamva mbebe
Kusiyana ndi ana ena iye !@#^i star
Ndinagwada kuthokoza Mbuye wodalitsa

Tinapita tonse kukagula ma dyper
Titagwirana manja pamalo panaipa
Tinakula koma we were getting tighter

Anthu otiyang'anan amadziwa
Timaitha


Nkhope yake inali brighter
Thupi lake linali lighter
Ndi nzeru anamudalitsa

Anatengera ine osakaika

Ndibwelere ndikagone (heh)

Mwina ndingalote nso (heh)
Ndingadzamukonde
Bola udzandibalire iweyoo


CHORUS
Ndinalota maloto otsekemera ine inde

Mwana wanga atafanana nawe Nde nde nde
Iwe
Ngati ndisadzuke

Usadzandikhumudwitse
Poti mtima wanga kukhala nawe wavomera


VERSE 2
Pali ponse
Anaoneka akalilombe

Ena anakondwa ena sanakondwe
Pawirife chikondi chinalipobe
Sichinachoke


Ndi za mbirimbiri
Zotilepheretsa kukhala awiri

Tiye tidzikondana mmene tiriri
Kunja kuli njoka wanga ndiwe basi
Ndikudziwa ndi zotheka eh

Kukonda iwe wekha eh
Chibwana ndaleka eh
Iwe mphete ndikuveka eh


Sweetie iwe ndine
Mphepo ingawombe tisasinthe

Limodzi tiwoloka mitsinje
Mpaka tikafike hey
Oh babie


CHORUS
Ndinalota maloto otsekera ine inde

Mwana wanga atafanana nawe Nde nde nde
Iwe
Ngati ndisadzuke

Usadzandikhumudwitse
Poti mtima wanga kukhala nawe wavomera


BRIDGE
No pain no gain
Kukusiya iwe no ways

Ngakhale asakondwe
Everything is gonna be okay


No pain no gain
Kukusiya iwe no ways
Ngakhale asakondwe

Everything is gonna be okay yeah

CHORUS

Ndinalota maloto otsekera ine inde
Mwana wanga atafanana nawe Nde nde nde
Iwe

Ngati ndisadzuke
Usadzandikhumudwitse
Poti mtima wanga kukhala nawe wavomera

Submit Corrections